Levitiko 26:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Chotero adzavomereza kuti iwo komanso makolo awo anayenda motsutsana nane,+ anandichimwira+ ndi kundichitira mosakhulupirika. Deuteronomo 4:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pamapeto pake, mawu amenewa akadzakwaniritsidwa pa inu, n’kukhala pamavuto aakulu, mudzabwereradi kwa Yehova Mulungu wanu+ ndi kumvetsera mawu ake.+
40 Chotero adzavomereza kuti iwo komanso makolo awo anayenda motsutsana nane,+ anandichimwira+ ndi kundichitira mosakhulupirika.
30 Pamapeto pake, mawu amenewa akadzakwaniritsidwa pa inu, n’kukhala pamavuto aakulu, mudzabwereradi kwa Yehova Mulungu wanu+ ndi kumvetsera mawu ake.+