Deuteronomo 30:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Adzachita zimenezi popeza udzamvera mawu a Yehova Mulungu wako ndi kusunga malamulo ake ndi mfundo zake zolembedwa m’buku ili la chilamulo,+ chifukwa udzabwerera kwa Yehova Mulungu wako ndi mtima wako wonse ndi moyo wako wonse.+ 2 Mbiri 33:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Manase anayamba kupemphera kwa Mulungu ndipo iye anamva kupembedzera kwake+ ndi pempho lake lopempha chifundo. Kenako anam’bwezera ku Yerusalemu ku ufumu wake,+ ndipo Manase anadziwa kuti Yehova ndiye Mulungu woona.+ Nehemiya 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mukadzabwerera kwa ine+ ndi kusunga malamulo anga,+ ngakhale anthu omwazikana a mtundu wanu atakhala kumalekezero a kumwamba, ndidzawasonkhanitsa kuchokera kumeneko+ ndi kuwabweretsa+ kumalo amene ndasankha kuikako dzina langa.’+
10 Adzachita zimenezi popeza udzamvera mawu a Yehova Mulungu wako ndi kusunga malamulo ake ndi mfundo zake zolembedwa m’buku ili la chilamulo,+ chifukwa udzabwerera kwa Yehova Mulungu wako ndi mtima wako wonse ndi moyo wako wonse.+
13 Manase anayamba kupemphera kwa Mulungu ndipo iye anamva kupembedzera kwake+ ndi pempho lake lopempha chifundo. Kenako anam’bwezera ku Yerusalemu ku ufumu wake,+ ndipo Manase anadziwa kuti Yehova ndiye Mulungu woona.+
9 Mukadzabwerera kwa ine+ ndi kusunga malamulo anga,+ ngakhale anthu omwazikana a mtundu wanu atakhala kumalekezero a kumwamba, ndidzawasonkhanitsa kuchokera kumeneko+ ndi kuwabweretsa+ kumalo amene ndasankha kuikako dzina langa.’+