Deuteronomo 30:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anthu a mtundu wanu obalalitsidwawo akadzakhala kumalekezero kwa thambo, Yehova Mulungu wanu adzakusonkhanitsani ndi kukutengani kumeneko.+ Salimo 106:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Tipulumutseni inu Yehova Mulungu wathu,+Tisonkhanitseni pamodzi kuchokera m’mitundu ina,+Kuti titamande dzina lanu loyera,+Ndi kuti tilankhule mokondwa pokutamandani.+ Yesaya 11:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iye adzakwezera chizindikiro mitundu ya anthu n’kusonkhanitsa Aisiraeli omwe anamwazikana.+ Ndipo adzasonkhanitsa pamodzi Ayuda omwe anabalalika, kuchokera kumalekezero anayi a dziko lapansi.+ Yeremiya 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno ndikadzawazula ndidzawachitiranso chifundo+ moti ndidzawabwezeretsa. Ndidzabwezeretsa aliyense pacholowa chake, ndiponso pamalo ake.”+
4 Anthu a mtundu wanu obalalitsidwawo akadzakhala kumalekezero kwa thambo, Yehova Mulungu wanu adzakusonkhanitsani ndi kukutengani kumeneko.+
47 Tipulumutseni inu Yehova Mulungu wathu,+Tisonkhanitseni pamodzi kuchokera m’mitundu ina,+Kuti titamande dzina lanu loyera,+Ndi kuti tilankhule mokondwa pokutamandani.+
12 Iye adzakwezera chizindikiro mitundu ya anthu n’kusonkhanitsa Aisiraeli omwe anamwazikana.+ Ndipo adzasonkhanitsa pamodzi Ayuda omwe anabalalika, kuchokera kumalekezero anayi a dziko lapansi.+
15 Ndiyeno ndikadzawazula ndidzawachitiranso chifundo+ moti ndidzawabwezeretsa. Ndidzabwezeretsa aliyense pacholowa chake, ndiponso pamalo ake.”+