Salimo 103:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 103 Tamanda Yehova, iwe moyo wanga.+Chilichonse mkati mwanga, chitamande dzina lake loyera.+ Salimo 105:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Nyadirani dzina lake loyera.+Mtima wa anthu ofunafuna Yehova usangalale.+