1 Mafumu 8:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 “Anthu anu Aisiraeli akagonja kwa adani+ awo chifukwa choti anali kukuchimwirani,+ ndiyeno akabwerera kwa inu+ n’kutamanda dzina lanu+ ndi kupemphera+ ndiponso kupempha kwa inu kuti muwachitire chifundo m’nyumba ino,+ Nehemiya 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamenepo mbewu ya Isiraeli inadzipatula+ kwa anthu onse osakhala Aisiraeli.+ Atatero anaimirira ndi kuulula+ machimo awo+ ndi zolakwa za makolo awo.+ Danieli 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ife tachimwa,+ talakwa, tachita zinthu zoipa ndipo takupandukirani.+ Tapatuka ndiponso tasiya malamulo anu ndi zigamulo zanu.+
33 “Anthu anu Aisiraeli akagonja kwa adani+ awo chifukwa choti anali kukuchimwirani,+ ndiyeno akabwerera kwa inu+ n’kutamanda dzina lanu+ ndi kupemphera+ ndiponso kupempha kwa inu kuti muwachitire chifundo m’nyumba ino,+
2 Pamenepo mbewu ya Isiraeli inadzipatula+ kwa anthu onse osakhala Aisiraeli.+ Atatero anaimirira ndi kuulula+ machimo awo+ ndi zolakwa za makolo awo.+
5 Ife tachimwa,+ talakwa, tachita zinthu zoipa ndipo takupandukirani.+ Tapatuka ndiponso tasiya malamulo anu ndi zigamulo zanu.+