1 Mafumu 8:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Anthu anu Aisiraeli akagonjetsedwa ndi adani awo chifukwa choti ankakuchimwirani,+ ndiyeno abwerera kwa inu nʼkutamanda dzina lanu+ mʼnyumbayi, kupemphera ndiponso kupempha kuti muwachitire chifundo,+
33 Anthu anu Aisiraeli akagonjetsedwa ndi adani awo chifukwa choti ankakuchimwirani,+ ndiyeno abwerera kwa inu nʼkutamanda dzina lanu+ mʼnyumbayi, kupemphera ndiponso kupempha kuti muwachitire chifundo,+