Levitiko 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “‘Ndipo akadziwa kuti wapalamula mlandu pa chilichonse mwa zimenezi, pamenepo aziulula+ kuti wachimwa motani. 2 Samueli 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamenepo Davide anauza+ Natani kuti: “Ndachimwira Yehova.”+ Ndiyeno Natani anauza Davide kuti: “Yehova wakukhululukira tchimo lako+ ndipo suufa.+ 2 Mbiri 30:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kuwonjezera apo, Hezekiya analankhula mokoma mtima+ kwa Alevi onse amene anali kutumikira Yehova mwanzeru.+ Anthuwo anachita phwando loikidwiratu kwa masiku 7.+ Anali kupereka nsembe zachiyanjano+ ndi kulapa+ kwa Yehova Mulungu wa makolo awo. Salimo 38:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pakuti ndinali kulankhula za cholakwa changa.+Ndipo ndinali kudera nkhawa za tchimo langa.+ Salimo 41:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma ine ndinati: “Inu Yehova, ndikomereni mtima.+Ndichiritseni, pakuti ndakuchimwirani.”+ Mateyu 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye anali kuwabatiza mumtsinje wa Yorodano,+ ndipo anthuwo anali kuulula machimo awo poyera.
5 “‘Ndipo akadziwa kuti wapalamula mlandu pa chilichonse mwa zimenezi, pamenepo aziulula+ kuti wachimwa motani.
13 Pamenepo Davide anauza+ Natani kuti: “Ndachimwira Yehova.”+ Ndiyeno Natani anauza Davide kuti: “Yehova wakukhululukira tchimo lako+ ndipo suufa.+
22 Kuwonjezera apo, Hezekiya analankhula mokoma mtima+ kwa Alevi onse amene anali kutumikira Yehova mwanzeru.+ Anthuwo anachita phwando loikidwiratu kwa masiku 7.+ Anali kupereka nsembe zachiyanjano+ ndi kulapa+ kwa Yehova Mulungu wa makolo awo.