Levitiko 26:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Chotero adzavomereza kuti iwo komanso makolo awo anayenda motsutsana nane,+ anandichimwira+ ndi kundichitira mosakhulupirika. Numeri 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Munthuyo aziulula+ tchimo lake limene wachita. Azipereka malipiro onse a mlandu wake, komanso aziwonjezerapo limodzi mwa magawo asanu a malipirowo.+ Azipereka malipirowo kwa munthu amene wam’lakwira. Yoswa 7:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tsopano Yoswa anauza Akani kuti: “Mwana wanga, chonde, lemekeza Yehova Mulungu wa Isiraeli,+ ulula kwa iye.+ Tandiuza+ chonde, n’chiyani chimene wachita? Usandibisire.”+ Ezara 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano vomerezani+ machimo anu kwa Yehova Mulungu wa makolo anu, ndipo chitani zomusangalatsa+ ndi kudzipatula kwa anthu a mitundu ina ndiponso kwa akazi achilendo.”+ Salimo 32:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pamapeto pake ndinaulula tchimo langa kwa inu, ndipo sindinabise cholakwa changa.+Ndinati: “Ndidzaulula kwa Yehova machimo anga.”+Ndipo inu munandikhululukira zolakwa zanga ndi machimo anga.+ [Seʹlah.] Miyambo 28:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Wobisa machimo ake zinthu sizidzamuyendera bwino,+ koma woulula n’kuwasiya adzachitiridwa chifundo.+ 1 Yohane 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mulungu ndi wokhulupirika ndiponso wolungama, chotero tikavomereza machimo athu,+ adzatikhululukira ndi kutiyeretsa ku ntchito zonse zoipa.+
40 Chotero adzavomereza kuti iwo komanso makolo awo anayenda motsutsana nane,+ anandichimwira+ ndi kundichitira mosakhulupirika.
7 Munthuyo aziulula+ tchimo lake limene wachita. Azipereka malipiro onse a mlandu wake, komanso aziwonjezerapo limodzi mwa magawo asanu a malipirowo.+ Azipereka malipirowo kwa munthu amene wam’lakwira.
19 Tsopano Yoswa anauza Akani kuti: “Mwana wanga, chonde, lemekeza Yehova Mulungu wa Isiraeli,+ ulula kwa iye.+ Tandiuza+ chonde, n’chiyani chimene wachita? Usandibisire.”+
11 Tsopano vomerezani+ machimo anu kwa Yehova Mulungu wa makolo anu, ndipo chitani zomusangalatsa+ ndi kudzipatula kwa anthu a mitundu ina ndiponso kwa akazi achilendo.”+
5 Pamapeto pake ndinaulula tchimo langa kwa inu, ndipo sindinabise cholakwa changa.+Ndinati: “Ndidzaulula kwa Yehova machimo anga.”+Ndipo inu munandikhululukira zolakwa zanga ndi machimo anga.+ [Seʹlah.]
13 Wobisa machimo ake zinthu sizidzamuyendera bwino,+ koma woulula n’kuwasiya adzachitiridwa chifundo.+
9 Mulungu ndi wokhulupirika ndiponso wolungama, chotero tikavomereza machimo athu,+ adzatikhululukira ndi kutiyeretsa ku ntchito zonse zoipa.+