Ezara 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho vomerezani machimo anu kwa Yehova Mulungu wa makolo anu ndipo chitani zomusangalatsa. Musiyane ndi anthu a mitundu ina ndiponso akazi achilendowa.”+
11 Choncho vomerezani machimo anu kwa Yehova Mulungu wa makolo anu ndipo chitani zomusangalatsa. Musiyane ndi anthu a mitundu ina ndiponso akazi achilendowa.”+