Ezara 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano vomerezani+ machimo anu kwa Yehova Mulungu wa makolo anu, ndipo chitani zomusangalatsa+ ndi kudzipatula kwa anthu a mitundu ina ndiponso kwa akazi achilendo.”+
11 Tsopano vomerezani+ machimo anu kwa Yehova Mulungu wa makolo anu, ndipo chitani zomusangalatsa+ ndi kudzipatula kwa anthu a mitundu ina ndiponso kwa akazi achilendo.”+