2 Akorinto 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chotero okondedwanu, popeza talonjezedwa zinthu zimenezi,+ tiyeni tidziyeretse+ ndipo tichotse chinthu chilichonse choipitsa thupi kapena mzimu,+ kwinaku tikukwaniritsa kukhala oyera poopa Mulungu.+ Tito 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iyeyo anadzipereka+ m’malo mwa ife kuti atilanditse+ ku moyo wochita zinthu zosamvera malamulo za mtundu uliwonse ndiponso kuti atiyeretse,+ kuti tikhale anthu akeake,+ odzipereka pa ntchito zabwino.+
7 Chotero okondedwanu, popeza talonjezedwa zinthu zimenezi,+ tiyeni tidziyeretse+ ndipo tichotse chinthu chilichonse choipitsa thupi kapena mzimu,+ kwinaku tikukwaniritsa kukhala oyera poopa Mulungu.+
14 Iyeyo anadzipereka+ m’malo mwa ife kuti atilanditse+ ku moyo wochita zinthu zosamvera malamulo za mtundu uliwonse ndiponso kuti atiyeretse,+ kuti tikhale anthu akeake,+ odzipereka pa ntchito zabwino.+