1 Timoteyo 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Akhale ogwira chikhulupiriro mwamphamvu, chimene ndi chinsinsi chopatulika+ cha Mulungu, ali ndi chikumbumtima choyera.+ 1 Yohane 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndipo aliyense amene ali ndi chiyembekezo chimenechi mwa iye, amadziyeretsa+ pakuti iye ndi woyera.+
9 Akhale ogwira chikhulupiriro mwamphamvu, chimene ndi chinsinsi chopatulika+ cha Mulungu, ali ndi chikumbumtima choyera.+
3 Ndipo aliyense amene ali ndi chiyembekezo chimenechi mwa iye, amadziyeretsa+ pakuti iye ndi woyera.+