Aefeso 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 ndiponso kuti anandiululira chinsinsi chopatulika,+ monga ndalemba kale mwachidule. Aefeso 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chinsinsi chimenechi n’chakuti anthu a mitundu ina nawonso akhale odzalandira cholowa, ndipo akhalenso ziwalo za thupi+ ndiponso otenga nawo mbali m’lonjezo pamodzi ndi ife,+ mogwirizana ndi Khristu Yesu kudzera mwa uthenga wabwino.
6 Chinsinsi chimenechi n’chakuti anthu a mitundu ina nawonso akhale odzalandira cholowa, ndipo akhalenso ziwalo za thupi+ ndiponso otenga nawo mbali m’lonjezo pamodzi ndi ife,+ mogwirizana ndi Khristu Yesu kudzera mwa uthenga wabwino.