Luka 24:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Ndipo ine ndidzatumiza kwa inu chimene Atate wanga analonjeza. Koma inu mukhalebe mumzindawu kufikira mutalandira mphamvu zochokera kumwamba.”+ Machitidwe 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma mzimu woyera ukadzafika pa inu, mudzalandira mphamvu.+ Pamenepo mudzakhala mboni+ zanga mu Yerusalemu,+ ku Yudeya konse ndi ku Samariya,+ mpaka kumalekezero a dziko lapansi.”+ Agalatiya 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Cholinga chake chinali chakuti mitundu ipeze madalitso amene Abulahamu analonjezedwa kudzera mwa Yesu Khristu,+ kuti tidzalandire mzimu wolonjezedwawo+ chifukwa cha chikhulupiriro chathu.+
49 Ndipo ine ndidzatumiza kwa inu chimene Atate wanga analonjeza. Koma inu mukhalebe mumzindawu kufikira mutalandira mphamvu zochokera kumwamba.”+
8 Koma mzimu woyera ukadzafika pa inu, mudzalandira mphamvu.+ Pamenepo mudzakhala mboni+ zanga mu Yerusalemu,+ ku Yudeya konse ndi ku Samariya,+ mpaka kumalekezero a dziko lapansi.”+
14 Cholinga chake chinali chakuti mitundu ipeze madalitso amene Abulahamu analonjezedwa kudzera mwa Yesu Khristu,+ kuti tidzalandire mzimu wolonjezedwawo+ chifukwa cha chikhulupiriro chathu.+