28 “Zimenezi zikadzachitika ndidzatsanulira mzimu wanga+ pa chamoyo chilichonse,+ ndipo ana anu aamuna ndi ana anu aakazi+ adzanenera. Amuna achikulire adzalota maloto ndipo anyamata adzaona masomphenya.
4 Pamene iye anali pa msonkhano limodzi ndi ophunzirawo, anawapatsa malangizo akuti: “Musatuluke mu Yerusalemu,+ koma muyembekezere chimene Atate analonjeza,+ chimene munamva kwa ine.