Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yohane 14:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Koma mthandizi, amene ndi mzimu woyera, amene Atate wanga adzatumiza m’dzina langa, adzakuphunzitsani zinthu zonse ndi kukukumbutsani zonse zimene ndinakuuzani.+

  • Machitidwe 6:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Chotero abale, fufuzani+ pakati panu amuna 7 a mbiri yabwino, amene ali ndi mzimu komanso nzeru zochuluka,+ kuti ife tiwaike kukhala oyang’anira ntchito yofunikayi.

  • 1 Petulo 1:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Zinaululidwa kwa iwo kuti sanali kudzitumikira okha,+ koma anali kutumikira inu mwa zinthu zimene tsopano zalengezedwa+ kwa inu. Zimenezi zalengezedwa kwa inu ndi olengeza uthenga wabwino, mwa mzimu woyera+ wotumizidwa kuchokera kumwamba. M’zinthu zimenezi angelo akulakalaka kusuzumiramo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena