Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Luka 24:49
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 49 Ndipo ine ndidzatumiza kwa inu chimene Atate wanga analonjeza. Koma inu mukhalebe mumzindawu kufikira mutalandira mphamvu zochokera kumwamba.”+

  • Yohane 15:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Akadzafika mthandizi amene ndidzamutumiza kuchokera kwa Atate,+ amene ndi mzimu wa choonadi wochokera kwa Atate, ameneyo adzandichitira umboni,+

  • Yohane 16:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Koma mthandiziyo akadzafika, amene ndi mzimu wa choonadi,+ adzakutsogolerani m’choonadi chonse. Pakuti sadzalankhula zongoganiza mwa iye yekha, koma adzalankhula zimene wazimva, ndipo adzalengeza kwa inu zinthu zimene zikubwera.+

  • 1 Yohane 2:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Inuyo, Mulungu anakudzozani ndi mzimu+ ndipo mzimu umenewo udakali mwa inu. Chotero simukufunikira wina aliyense kuti azikuphunzitsani,+ koma popeza kuti munadzozedwadi moona+ osati monama, chifukwa cha kudzozedwako, mukuphunzitsidwa zinthu zonse.+ Monga mmene mwaphunzitsidwira, pitirizani kukhala ogwirizana+ naye.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena