Yohane 16:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma kunena zoona, ndikupita kuti inu mupindule. Pakuti ngati sindipita, ndiye kuti mthandizi+ uja sabwera kwa inu. Koma ndikapita, ndikamutumiza kwa inu.
7 Koma kunena zoona, ndikupita kuti inu mupindule. Pakuti ngati sindipita, ndiye kuti mthandizi+ uja sabwera kwa inu. Koma ndikapita, ndikamutumiza kwa inu.