Yohane 16:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kunena zoona, ndikupita kuti inu mupindule. Chifukwa ngati sindipita ndiye kuti mthandizi uja+ sabwera kwa inu. Koma ndikapita ndikamutumiza kwa inu. Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:7 Yesu—Ndi Njira, tsa. 278 Nsanja ya Olonda,4/15/2008, tsa. 329/15/1992, ptsa. 15-169/1/1990, tsa. 8
7 Kunena zoona, ndikupita kuti inu mupindule. Chifukwa ngati sindipita ndiye kuti mthandizi uja+ sabwera kwa inu. Koma ndikapita ndikamutumiza kwa inu.
16:7 Yesu—Ndi Njira, tsa. 278 Nsanja ya Olonda,4/15/2008, tsa. 329/15/1992, ptsa. 15-169/1/1990, tsa. 8