1 Yohane 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ameneyu ndi Yesu Khristu, amene anabwera kudzera mwa madzi ndi magazi. Sanabwere kudzera mwa madzi+ okha, koma anabwera kudzera mwa madzi ndi magazi.+ Ndipo mzimu+ ndi umene ukuchitira umboni, chifukwa mzimu ndiwo choonadi.
6 Ameneyu ndi Yesu Khristu, amene anabwera kudzera mwa madzi ndi magazi. Sanabwere kudzera mwa madzi+ okha, koma anabwera kudzera mwa madzi ndi magazi.+ Ndipo mzimu+ ndi umene ukuchitira umboni, chifukwa mzimu ndiwo choonadi.