Machitidwe 20:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mukhale tcheru ndi kuyang’anira+ gulu lonse la nkhosa,+ limene mzimu woyera wakuikani pakati pawo kukhala oyang’anira,+ kuti muwete mpingo wa Mulungu,+ umene anaugula ndi magazi+ a Mwana wake weniweni. Aefeso 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kudzera mwa iyeyu, tinamasulidwa ndi dipo* la magazi+ ake, inde, takhululukidwa+ machimo athu, malinga ndi chuma cha kukoma mtima kwake kwakukulu.+ Aheberi 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Inde, pafupifupi zinthu zonse zimayeretsedwa ndi magazi+ malinga ndi Chilamulo, ndipo popanda kukhetsa magazi+ anthu sangakhululukidwe machimo awo.+ 1 Petulo 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma munamasulidwa ndi magazi amtengo wapatali,+ monga a nkhosa yopanda chilema ndi yopanda mawanga,+ magazi a Khristu.+
28 Mukhale tcheru ndi kuyang’anira+ gulu lonse la nkhosa,+ limene mzimu woyera wakuikani pakati pawo kukhala oyang’anira,+ kuti muwete mpingo wa Mulungu,+ umene anaugula ndi magazi+ a Mwana wake weniweni.
7 Kudzera mwa iyeyu, tinamasulidwa ndi dipo* la magazi+ ake, inde, takhululukidwa+ machimo athu, malinga ndi chuma cha kukoma mtima kwake kwakukulu.+
22 Inde, pafupifupi zinthu zonse zimayeretsedwa ndi magazi+ malinga ndi Chilamulo, ndipo popanda kukhetsa magazi+ anthu sangakhululukidwe machimo awo.+
19 Koma munamasulidwa ndi magazi amtengo wapatali,+ monga a nkhosa yopanda chilema ndi yopanda mawanga,+ magazi a Khristu.+