Ekisodo 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Nkhosa yanuyo ikhale yopanda chilema,+ yamphongo, yachaka chimodzi.+ Mungatenge mwana wa nkhosa kapena wa mbuzi. Levitiko 22:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Nyama iliyonse yachilema musaipereke nsembe,+ chifukwa Mulungu sadzakuyanjani. Yohane 1:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Tsiku lotsatira anaona Yesu akubwera kwa iye, ndipo anati: “Taonani, Mwanawankhosa+ wa Mulungu amene akuchotsa uchimo+ wa dziko!+
5 Nkhosa yanuyo ikhale yopanda chilema,+ yamphongo, yachaka chimodzi.+ Mungatenge mwana wa nkhosa kapena wa mbuzi.
29 Tsiku lotsatira anaona Yesu akubwera kwa iye, ndipo anati: “Taonani, Mwanawankhosa+ wa Mulungu amene akuchotsa uchimo+ wa dziko!+