Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 12:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Uzani khamu lonse la Isiraeli kuti, ‘Pa tsiku la 10 la mwezi uno mabanja onse ochokera mwa kholo limodzi atenge nkhosa imodziimodzi,+ banja lililonse litenge nkhosa imodzi.

  • Yesaya 53:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Iye anapanikizidwa+ ndipo analola kuti asautsidwe,+ koma sanatsegule pakamwa pake. Anatengedwa ngati nkhosa yopita kokaphedwa,+ ndipo mofanana ndi nkhosa yaikazi imene imakhala chete akamaimeta ubweya, nayenso sanatsegule pakamwa pake.+

  • 1 Akorinto 5:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Chotsani chofufumitsa chakalecho, kuti mukhale mtanda watsopano,+ popeza ndinu opanda chofufumitsa. Pakuti Khristu+ waperekedwa+ monga nsembe yathu ya pasika.+

  • 1 Petulo 1:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Koma munamasulidwa ndi magazi amtengo wapatali,+ monga a nkhosa yopanda chilema ndi yopanda mawanga,+ magazi a Khristu.+

  • Chivumbulutso 5:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Kenako ndinaona mwana wa nkhosa+ wooneka ngati wophedwa,+ ataimirira pafupi ndi mpando wachifumu+ uja ndi zamoyo zinayi, ndi pakati pa akulu aja.+ Iye anali ndi nyanga 7, ndi maso 7. Maso amenewo akuimira mizimu 7 ya Mulungu,+ imene yatumizidwa m’dziko lonse lapansi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena