Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Chivumbulutso 5
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Chivumbulutso 5:1

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eze 2:10
  • +Chv 4:2
  • +Yes 29:11; Da 12:9

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 82-83

Chivumbulutso 5:2

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 82-83

Chivumbulutso 5:3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 82-83

Chivumbulutso 5:4

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mt 24:36; Mac 1:7

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 82-83

Chivumbulutso 5:5

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Ge 49:9; Ahe 7:14
  • +Yes 11:1; Aro 15:12
  • +2Sa 7:12; Chv 22:16
  • +Yoh 16:33

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    “Wotsatira Wanga,” ptsa. 35-36

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 83-84

    Nsanja ya Olonda,

    8/15/1994, tsa. 31

Chivumbulutso 5:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 53:7; Yoh 1:29; 1Pe 1:19
  • +Yoh 19:30; Chv 5:12
  • +Aef 1:20
  • +Aef 1:22
  • +Chv 1:4

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    1/15/2009, tsa. 30

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 55, 84-85

Chivumbulutso 5:7

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 47:8; Yes 6:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 85

Chivumbulutso 5:8

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 5:14; 19:4
  • +2Mb 29:25; Chv 15:2
  • +Sl 141:2; Chv 8:4
  • +Akl 4:2

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 85-87

Chivumbulutso 5:9

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 33:3; 144:9; Yes 42:10; Chv 14:3
  • +Mt 26:28; Ahe 9:12; 1Pe 1:19
  • +1Ak 6:20
  • +Chv 14:4

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 31

    Nsanja ya Olonda (Yogawira),

    No. 6 2016, tsatsa. 6-7

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 85-88

    Mtendere Weniweni, ptsa. 65-66

Chivumbulutso 5:10

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Lu 12:32; 22:29; Ahe 12:28
  • +Chv 1:6
  • +Eks 19:6; 1Pe 2:9; Chv 20:6
  • +Mt 19:28; Chv 20:4; 22:5

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 31

    Nsanja ya Olonda (Yogawira),

    No. 6 2016, tsatsa. 6-7

    Nsanja ya Olonda,

    8/15/2006, ptsa. 6-7

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 87-88

Chivumbulutso 5:11

Mawu a M'munsi

  • *

    Kapena kuti, “10,000 kuchulukitsa ndi ma 10,000.”

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +De 33:2; Ahe 12:22; Yuda 14
  • +Da 7:10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 24

    Galamukani!,

    4/2011, tsa. 29

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 88

    Nsanja ya Olonda,

    5/15/1987, tsa. 12

Chivumbulutso 5:12

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 53:7; Chv 5:6
  • +Mt 28:18

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 88

Chivumbulutso 5:13

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Afi 2:10
  • +1Mf 22:19; Chv 4:2
  • +Yoh 1:29; Chv 7:17
  • +Yoh 5:23; 1Ti 6:16
  • +1Pe 4:11

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    3/2017, ptsa. 8-9

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 88-89

Chivumbulutso 5:14

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 7:11
  • +Mt 4:10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 89

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

Chiv. 5:1Eze 2:10
Chiv. 5:1Chv 4:2
Chiv. 5:1Yes 29:11; Da 12:9
Chiv. 5:4Mt 24:36; Mac 1:7
Chiv. 5:5Ge 49:9; Ahe 7:14
Chiv. 5:5Yes 11:1; Aro 15:12
Chiv. 5:52Sa 7:12; Chv 22:16
Chiv. 5:5Yoh 16:33
Chiv. 5:6Yes 53:7; Yoh 1:29; 1Pe 1:19
Chiv. 5:6Yoh 19:30; Chv 5:12
Chiv. 5:6Aef 1:20
Chiv. 5:6Aef 1:22
Chiv. 5:6Chv 1:4
Chiv. 5:7Sl 47:8; Yes 6:1
Chiv. 5:8Chv 5:14; 19:4
Chiv. 5:82Mb 29:25; Chv 15:2
Chiv. 5:8Sl 141:2; Chv 8:4
Chiv. 5:8Akl 4:2
Chiv. 5:9Sl 33:3; 144:9; Yes 42:10; Chv 14:3
Chiv. 5:9Mt 26:28; Ahe 9:12; 1Pe 1:19
Chiv. 5:91Ak 6:20
Chiv. 5:9Chv 14:4
Chiv. 5:10Lu 12:32; 22:29; Ahe 12:28
Chiv. 5:10Chv 1:6
Chiv. 5:10Eks 19:6; 1Pe 2:9; Chv 20:6
Chiv. 5:10Mt 19:28; Chv 20:4; 22:5
Chiv. 5:11De 33:2; Ahe 12:22; Yuda 14
Chiv. 5:11Da 7:10
Chiv. 5:12Yes 53:7; Chv 5:6
Chiv. 5:12Mt 28:18
Chiv. 5:13Afi 2:10
Chiv. 5:131Mf 22:19; Chv 4:2
Chiv. 5:13Yoh 1:29; Chv 7:17
Chiv. 5:13Yoh 5:23; 1Ti 6:16
Chiv. 5:131Pe 4:11
Chiv. 5:14Chv 7:11
Chiv. 5:14Mt 4:10
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano (nwt)
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
  • 14
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Chivumbulutso 5:1-14

Chivumbulutso

5 Kenako, ndinaona mpukutu wolembedwa mkati ndi kunja komwe,+ uli m’dzanja lamanja la Iye wokhala pampando wachifumu.+ Unali womatidwa+ mwamphamvu ndi zidindo 7 zomatira. 2 Ndipo ndinaona mngelo wamphamvu akulengeza ndi mawu okweza kuti: “Ndani ali woyenera kumatula zidindo zimene amatira mpukutuwu ndi kuutsegula?” 3 Koma sipanapezeke ndi mmodzi yemwe, kaya kumwamba, padziko lapansi, kapena pansi pa nthaka, wotha kutsegula mpukutuwo kapena kuyang’anamo ndi kuuwerenga. 4 Choncho ine ndinalira kwambiri chifukwa sipanapezeke wina aliyense woyenera kutsegula mpukutuwo, kapena kuyang’anamo ndi kuuwerenga.+ 5 Koma mmodzi wa akulu aja anandiuza kuti: “Tonthola. Taona! Mkango wa fuko la Yuda,+ muzu+ wa Davide,+ anapambana pa nkhondo+ moti iye ndiye woyenera kumatula zidindo 7 zimene amatira mpukutuwo ndi kuutsegula.”

6 Kenako ndinaona mwana wa nkhosa+ wooneka ngati wophedwa,+ ataimirira pafupi ndi mpando wachifumu+ uja ndi zamoyo zinayi, ndi pakati pa akulu aja.+ Iye anali ndi nyanga 7, ndi maso 7. Maso amenewo akuimira mizimu 7 ya Mulungu,+ imene yatumizidwa m’dziko lonse lapansi. 7 Iye anapita, ndipo nthawi yomweyo anatenga mpukutu umene unali kudzanja lamanja la Iye wokhala pampando wachifumu.+ 8 Atatenga mpukutuwo, zamoyo zinayi ndi akulu 24 aja+ anagwada ndi kuwerama pamaso pa Mwanawankhosa. Aliyense wa iwo anali ndi zeze woimbira+ ndi mbale yagolide yodzaza ndi zofukiza. Zofukizazo+ zikuimira mapemphero+ a oyera. 9 Iwo anali kuimba nyimbo yatsopano,+ yakuti: “Inu ndinu woyenera kutenga mpukutuwo ndi kumatula zidindo zake zomatira, chifukwa munaphedwa, ndipo ndi magazi anu,+ munagula+ anthu kuti atumikire Mulungu.+ Anthu ochokera mu fuko lililonse, chinenero chilichonse, mtundu uliwonse, ndi dziko lililonse. 10 Ndipo munawasandutsa mafumu+ ndi ansembe+ a Mulungu wathu,+ moti adzakhala mafumu+ olamulira dziko lapansi.”

11 Kenako, ndinaona ndi kumva mawu a angelo ambiri atazungulira mpando wachifumu limodzi ndi zamoyo zija ndi akulu aja. Chiwerengero chawo chinali miyanda kuchulukitsa ndi miyanda*+ ndiponso masauzande kuchulukitsa ndi masauzande.+ 12 Iwo anali kunena mofuula kuti: “Mwanawankhosa amene anaphedwa+ ndiye woyenera kulandira mphamvu, chuma, nzeru, nyonga, ulemu, ulemerero, ndi madalitso.”+

13 Ndipo cholengedwa chilichonse chakumwamba, padziko lapansi,+ pansi pa nthaka, panyanja, ndi zinthu zonse za mmenemo, ndinazimva zikunena kuti: “Iye wokhala pampando wachifumu,+ ndi Mwanawankhosa,+ atamandidwe ndiponso alandire ulemu,+ ulemerero,+ ndi mphamvu, kwamuyaya.” 14 Ndiyeno zamoyo zinayi zija zinati: “Ame!” Ndipo akulu aja+ anagwada n’kuwerama ndi kulambira.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena