Chivumbulutso 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiyeno zamoyo zinayi zija zinati: “Ame!” Ndipo akulu aja+ anagwada n’kuwerama ndi kulambira.+ Chivumbulutso 19:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndipo akulu+ 24 ndi zamoyo zinayi zija,+ anagwada pansi ndi kuwerama, n’kulambira Mulungu wokhala+ pampando wachifumu, ndi mawu akuti: “Ame! Tamandani Ya,+ anthu inu!”
4 Ndipo akulu+ 24 ndi zamoyo zinayi zija,+ anagwada pansi ndi kuwerama, n’kulambira Mulungu wokhala+ pampando wachifumu, ndi mawu akuti: “Ame! Tamandani Ya,+ anthu inu!”