Chivumbulutso 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Atatenga mpukutuwo, angelo 4 ndi akulu 24 aja+ anagwada nʼkuwerama pamaso pa Mwanawankhosa. Aliyense wa iwo anali ndi zeze komanso mbale yagolide yodzaza ndi zofukiza. (Zofukizazo zikuimira mapemphero a oyera.)+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:8 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 85-87
8 Atatenga mpukutuwo, angelo 4 ndi akulu 24 aja+ anagwada nʼkuwerama pamaso pa Mwanawankhosa. Aliyense wa iwo anali ndi zeze komanso mbale yagolide yodzaza ndi zofukiza. (Zofukizazo zikuimira mapemphero a oyera.)+