Yohane 5:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 kuti onse alemekeze Mwana+ monga mmene amalemekezera Atate. Wosalemekeza Mwana salemekeza Atate amene anamutuma.+ 1 Timoteyo 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iye yekha ndiye amene ali ndi moyo wosakhoza kufa,+ amene amakhala m’kuwala kosafikirika.+ Palibe munthu ndi mmodzi yemwe amene anamuonapo kapena amene angamuone.+ Iye apatsidwe ulemu+ ndipo mphamvu zake zikhalebe kosatha. Ame.
23 kuti onse alemekeze Mwana+ monga mmene amalemekezera Atate. Wosalemekeza Mwana salemekeza Atate amene anamutuma.+
16 Iye yekha ndiye amene ali ndi moyo wosakhoza kufa,+ amene amakhala m’kuwala kosafikirika.+ Palibe munthu ndi mmodzi yemwe amene anamuonapo kapena amene angamuone.+ Iye apatsidwe ulemu+ ndipo mphamvu zake zikhalebe kosatha. Ame.