1 Timoteyo 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iyeyo ali ndi moyo woti sungafe+ ndipo amakhala pamalo owala kwambiri moti palibe munthu angafikepo.+ Palibenso munthu amene anamuonapo kapena amene angamuone.+ Iye apatsidwe ulemu ndipo mphamvu zake zikhalebe mpaka kalekale. Ame. 1 Timoteyo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:16 Nsanja ya Olonda,9/15/2008, tsa. 319/1/2005, tsa. 27 Galamukani!,9/8/1990, tsa. 21
16 Iyeyo ali ndi moyo woti sungafe+ ndipo amakhala pamalo owala kwambiri moti palibe munthu angafikepo.+ Palibenso munthu amene anamuonapo kapena amene angamuone.+ Iye apatsidwe ulemu ndipo mphamvu zake zikhalebe mpaka kalekale. Ame.