15 Zimenezi zikumveka bwino tsopano chifukwa pabwera wansembe wina+ wofanana ndi Melekizedeki.+ 16 Iyeyu wakhala wansembe, osati mogwirizana ndi malamulo, amene amadalira zinthu zapadziko lapansi, koma mogwirizana ndi mphamvu ya moyo umene sungawonongeke.+