Aroma 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tikudziwa kuti popeza Khristu waukitsidwa,+ sadzafanso+ ndipo imfa sikumulamuliranso ngati mfumu. 1 Timoteyo 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iyeyo ali ndi moyo woti sungafe+ ndipo amakhala pamalo owala kwambiri moti palibe munthu angafikepo.+ Palibenso munthu amene anamuonapo kapena amene angamuone.+ Iye apatsidwe ulemu ndipo mphamvu zake zikhalebe mpaka kalekale. Ame.
16 Iyeyo ali ndi moyo woti sungafe+ ndipo amakhala pamalo owala kwambiri moti palibe munthu angafikepo.+ Palibenso munthu amene anamuonapo kapena amene angamuone.+ Iye apatsidwe ulemu ndipo mphamvu zake zikhalebe mpaka kalekale. Ame.