-
Chivumbulutso 1:17, 18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Nditamuona, ndinagwera pamapazi ake ngati kuti ndafa.
Ndipo anandigwira ndi dzanja lake lamanja nʼkundiuza kuti: “Usachite mantha. Ine ndine Woyamba+ ndi Womaliza,+ 18 ndiponso wamoyo.+ Ndinali wakufa,+ koma taona, ndili ndi moyo ndipo ndidzakhala ndi moyo mpaka kalekale,+ komanso ndili ndi makiyi a imfa ndi a Manda.*+
-