Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Chivumbulutso 4
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Chivumbulutso 4:1

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eks 19:16; Chv 1:10
  • +Ge 28:12; Chv 11:12
  • +Da 2:28; Chv 1:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 74

Chivumbulutso 4:2

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Mf 22:19; Yes 6:1
  • +Sl 11:4; Mac 7:55
  • +Eze 1:26; Da 7:9

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 74-76

Chivumbulutso 4:3

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Yo 1:5
  • +Chv 21:11
  • +Ge 9:13
  • +Eks 28:17

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yogawira),

    No. 6 2016, tsa. 4

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 76

    Nsanja ya Olonda,

    3/15/2005, tsa. 31

Chivumbulutso 4:4

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 3:21; 20:4
  • +1Mb 24:1, 18; Lu 1:5
  • +Chv 1:6; 4:10
  • +Chv 6:11; 19:8
  • +1Pe 5:4

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 76-77, 102-103, 288-289

    Nsanja ya Olonda,

    7/1/1995, tsa. 13

Chivumbulutso 4:5

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yob 38:35; Eze 1:13
  • +Eks 19:16; 20:18
  • +Eks 25:31; 40:24
  • +Chv 1:4; 5:6

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    1/15/2009, tsa. 30

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 77-79

Chivumbulutso 4:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eks 30:18; 1Mf 7:23
  • +Eze 1:5; Chv 4:9

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 79-80

Chivumbulutso 4:7

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2Sa 17:10; Miy 28:1; Yes 31:4
  • +1Mf 7:25; Chv 6:3
  • +Chv 6:5
  • +Chv 6:7
  • +Yob 39:29; Eze 1:10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 80-81

Chivumbulutso 4:8

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 5:8
  • +Yes 6:2
  • +Miy 15:3; Eze 1:18; 10:12; Ahe 4:13
  • +Yes 6:3; Lu 1:49
  • +Eks 6:3; Chv 11:17; 15:3
  • +Eks 3:14; Chv 1:4

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 4

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 81, 129

    Nsanja ya Olonda,

    5/1/1986, tsa. 15

Chivumbulutso 4:9

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 92:1
  • +Sl 47:8; Chv 21:5
  • +Sl 90:2; Da 4:34; 12:7

Chivumbulutso 4:10

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 5:8
  • +1Mb 16:29; Sl 95:6; Chv 19:10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 81

Chivumbulutso 4:11

Mawu a M'munsi

  • *

    Onani Zakumapeto 2.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 5:13
  • +Mt 5:16; Chv 14:7
  • +1Ti 1:17; Chv 7:12; 11:17; 12:10
  • +Aef 3:9; Chv 10:6
  • +Mt 6:10; 26:39; 1Pe 4:2; 1Yo 2:17
  • +Ge 2:3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 4

    Nsanja ya Olonda,

    12/1/2008, tsa. 31

    12/1/1999, ptsa. 10-11

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 81

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

Chiv. 4:1Eks 19:16; Chv 1:10
Chiv. 4:1Ge 28:12; Chv 11:12
Chiv. 4:1Da 2:28; Chv 1:1
Chiv. 4:21Mf 22:19; Yes 6:1
Chiv. 4:2Sl 11:4; Mac 7:55
Chiv. 4:2Eze 1:26; Da 7:9
Chiv. 4:31Yo 1:5
Chiv. 4:3Chv 21:11
Chiv. 4:3Ge 9:13
Chiv. 4:3Eks 28:17
Chiv. 4:4Chv 3:21; 20:4
Chiv. 4:41Mb 24:1, 18; Lu 1:5
Chiv. 4:4Chv 1:6; 4:10
Chiv. 4:4Chv 6:11; 19:8
Chiv. 4:41Pe 5:4
Chiv. 4:5Yob 38:35; Eze 1:13
Chiv. 4:5Eks 19:16; 20:18
Chiv. 4:5Eks 25:31; 40:24
Chiv. 4:5Chv 1:4; 5:6
Chiv. 4:6Eks 30:18; 1Mf 7:23
Chiv. 4:6Eze 1:5; Chv 4:9
Chiv. 4:72Sa 17:10; Miy 28:1; Yes 31:4
Chiv. 4:71Mf 7:25; Chv 6:3
Chiv. 4:7Chv 6:5
Chiv. 4:7Chv 6:7
Chiv. 4:7Yob 39:29; Eze 1:10
Chiv. 4:8Chv 5:8
Chiv. 4:8Yes 6:2
Chiv. 4:8Miy 15:3; Eze 1:18; 10:12; Ahe 4:13
Chiv. 4:8Yes 6:3; Lu 1:49
Chiv. 4:8Eks 6:3; Chv 11:17; 15:3
Chiv. 4:8Eks 3:14; Chv 1:4
Chiv. 4:9Sl 92:1
Chiv. 4:9Sl 47:8; Chv 21:5
Chiv. 4:9Sl 90:2; Da 4:34; 12:7
Chiv. 4:10Chv 5:8
Chiv. 4:101Mb 16:29; Sl 95:6; Chv 19:10
Chiv. 4:11Chv 5:13
Chiv. 4:11Mt 5:16; Chv 14:7
Chiv. 4:111Ti 1:17; Chv 7:12; 11:17; 12:10
Chiv. 4:11Aef 3:9; Chv 10:6
Chiv. 4:11Mt 6:10; 26:39; 1Pe 4:2; 1Yo 2:17
Chiv. 4:11Ge 2:3
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano (nwt)
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Chivumbulutso 4:1-11

Chivumbulutso

4 Zimenezi zitatha, nditayang’ana ndinaona khomo lotseguka kumwamba. Ndipo mawu oyamba amene ndinawamva akundilankhula anali ngati kulira kwa lipenga.+ Mawuwo anali akuti: “Kwera kumwamba kuno,+ ndikuonetse zinthu zimene ziyenera kuchitika.”+ 2 Zitatero, nthawi yomweyo ndinakhala mumphamvu ya mzimu, ndipo mpando wachifumu+ unaoneka uli pamalo ake kumwamba,+ wina atakhalapo.+ 3 Wokhala pampandoyo, anali wooneka+ ngati mwala wa yasipi,+ ndi mwala wofiira wamtengo wapatali. Utawaleza+ wooneka ngati mwala wa emarodi+ unazungulira mpando wachifumuwo.

4 Kuzungulira mpando wachifumuwo, panalinso mipando yachifumu yokwanira 24. Pamipando yachifumuyo,+ ndinaona patakhala akulu+ 24+ ovala malaya akunja oyera,+ ndi zisoti zachifumu+ zagolide pamitu pawo. 5 Kumpando wachifumuko kunali kutuluka mphezi,+ mawu, ndi mabingu.+ Panalinso nyale+ zamoto 7 zikuyaka patsogolo pa mpando wachifumuwo. Zimenezo zikuimira mizimu 7+ ya Mulungu. 6 Patsogolo pa mpando wachifumuwo, panali nyanja yoyera mbee! ngati galasi,+ yooneka ngati mwala wa kulusitalo.

Pakati m’pakati pa mpando wachifumuwo, ndiponso mouzungulira, panali zamoyo zinayi+ zokhala ndi maso ambirimbiri, kutsogolo ndi kumbuyo komwe. 7 Chamoyo choyamba chinali ngati mkango.+ Chamoyo chachiwiri chinali ngati mwana wa ng’ombe wamphongo.+ Chamoyo+ chachitatu chinali ndi nkhope ngati ya munthu, ndipo chamoyo+ chachinayi chinali ngati chiwombankhanga+ chimene chikuuluka. 8 Zamoyo zinayizo,+ chilichonse chinali ndi mapiko 6.+ Zinali ndi maso thupi lonse ngakhalenso kunsi kwa mapiko.+ Zamoyo zimenezi sizinali kupuma usana ndi usiku. Zinali kunena kuti: “Woyera, woyera, woyera ndiye Yehova+ Mulungu, Wamphamvuyonse,+ amene analipo, amene alipo,+ ndi amene akubwera.”

9 Nthawi zonse zamoyozo zikamapereka ulemerero, ndi ulemu, ndiponso zikamayamikira+ Wokhala pampando wachifumuyo,+ Iye amene adzakhalabe ndi moyo kwamuyaya,+ 10 akulu 24 aja+ anali kugwada ndi kuwerama pamaso pa Wokhala pampando wachifumuyo, ndi kulambira+ wokhala ndi moyo kwamuyayayo. Iwo anali kuponya pansi zisoti zawo zachifumu pamaso pa mpando wachifumuwo, ndi kunena kuti: 11 “Ndinu woyenera, inu Yehova* Mulungu wathu wamphamvu,+ kulandira ulemerero+ ndi ulemu,+ chifukwa munalenga zinthu zonse,+ ndipo mwa kufuna kwanu,+ zinakhalapo ndipo zinalengedwa.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena