Chivumbulutso 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 n’kutipanga kukhala mafumu+ ndi ansembe+ kwa Mulungu wake ndi Atate wake, kwa iyeyo kukhale ulemerero ndi mphamvu kwamuyaya.+ Ame. Chivumbulutso 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 akulu 24 aja+ anali kugwada ndi kuwerama pamaso pa Wokhala pampando wachifumuyo, ndi kulambira+ wokhala ndi moyo kwamuyayayo. Iwo anali kuponya pansi zisoti zawo zachifumu pamaso pa mpando wachifumuwo, ndi kunena kuti:
6 n’kutipanga kukhala mafumu+ ndi ansembe+ kwa Mulungu wake ndi Atate wake, kwa iyeyo kukhale ulemerero ndi mphamvu kwamuyaya.+ Ame.
10 akulu 24 aja+ anali kugwada ndi kuwerama pamaso pa Wokhala pampando wachifumuyo, ndi kulambira+ wokhala ndi moyo kwamuyayayo. Iwo anali kuponya pansi zisoti zawo zachifumu pamaso pa mpando wachifumuwo, ndi kunena kuti: