Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Chivumbulutso 1
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Chivumbulutso 1:1

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 14:6; Aga 1:12
  • +Da 2:28; Yoh 12:49
  • +Amo 3:7; Chv 7:3; 22:6
  • +Chv 1:19
  • +Chv 22:16
  • +Mac 2:22
  • +Mt 10:2; Mko 1:19; Yoh 21:20

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2022, tsa. 2

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 15-17

    Nsanja ya Olonda,

    12/1/1999, ptsa. 15, 19

    11/1/1999, tsa. 6

Chivumbulutso 1:2

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 1:9
  • +Chv 22:20

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 16-17

Chivumbulutso 1:3

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yoh 13:17
  • +Sl 1:2; 1Ti 4:13
  • +Chv 22:18
  • +Lu 11:28; Yak 1:22
  • +Da 8:19; Chv 22:10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    1/15/2009, tsa. 31

    12/1/1999, ptsa. 14-19

    4/1/1989, ptsa. 10-11

    12/15/1988, ptsa. 10-11

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 6, 17

Chivumbulutso 1:4

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 1:11
  • +Eks 3:14; Chv 1:8; 4:8; 11:17
  • +Chv 4:5

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    1/15/2009, tsa. 30

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 18

Chivumbulutso 1:5

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 89:37; Chv 3:14
  • +Akl 1:18
  • +Sl 89:27; 1Ti 6:15; Chv 19:16
  • +Yoh 15:9
  • +Ahe 9:14; 1Pe 1:19; 1Yo 1:7

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 18-19

    Nsanja ya Olonda,

    12/1/1999, tsa. 10

Chivumbulutso 1:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eks 19:6; Lu 22:29
  • +1Pe 2:5; Chv 5:10; 20:6
  • +1Ti 6:16

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 19

Chivumbulutso 1:7

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Da 7:13; Mt 26:64; Mko 13:26; Mac 1:11; 1At 4:17; Chv 14:14
  • +Aef 1:18
  • +Mt 27:49
  • +Mt 24:30

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Ufumu wa Mulungu Ukulamulira, tsa. 226

    Nsanja ya Olonda,

    3/15/2007, ptsa. 3, 5

    5/1/1993, ptsa. 22-23

    10/1/1992, ptsa. 15-16

    1/1/1988, tsa. 18

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 19-20

    Kukhala ndi Moyo Kosatha, tsa. 146

    Kukambitsirana, ptsa. 163-164

Chivumbulutso 1:8

Mawu a M'munsi

  • *

    Onani Matanthauzo a Mawu Ena.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 48:12; Chv 21:6; 22:13
  • +Chv 1:4
  • +Ge 17:1; Eks 6:3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2136

    Nsanja ya Olonda,

    1/15/2009, ptsa. 30-31

    12/1/1999, tsa. 10

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 20

Chivumbulutso 1:9

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mt 24:9; Ahe 10:33; Chv 2:10
  • +Aro 8:17
  • +Lu 12:32
  • +Mt 10:22; 2Ti 2:12
  • +Mac 1:8

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 20-21

    Nsanja ya Olonda,

    12/1/1999, ptsa. 14-15

Chivumbulutso 1:10

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Mb 28:12; Mt 22:43
  • +Eze 40:2; 2Ak 12:2
  • +1Ak 1:8; 5:5
  • +Chv 1:15

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2022, ptsa. 2-3

    Yesu—Ndi Njira, tsa. 313

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 22-24

    Nsanja ya Olonda,

    5/15/2003, tsa. 10

    12/15/1997, tsa. 11

    4/15/1991, ptsa. 26-27

    4/1/1989, ptsa. 11-12

    12/15/1988, tsa. 11

    10/15/1988, tsa. 10

Chivumbulutso 1:11

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Hab 2:2
  • +Chv 1:4
  • +Aef 1:1; Chv 2:1
  • +Chv 2:8
  • +Chv 2:12
  • +Mac 16:14; Chv 2:18
  • +Chv 3:1
  • +Chv 3:7
  • +Akl 4:16; Chv 3:14

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Nsanja ya Olonda,

    1/15/2009, tsa. 30

    8/15/2007, ptsa. 9, 11

    4/1/1989, tsa. 11

    12/15/1988, tsa. 11

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 23-24

    ‘Dziko Lokoma’, tsa. 33

    Sukulu ya Utumiki Wateokalase (1999), ptsa. 15-16

    Kukambitsirana, tsa. 399

Chivumbulutso 1:12

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2Mb 4:7; Chv 1:20

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 25, 28-29

Chivumbulutso 1:13

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Da 7:13; Chv 14:14

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 25

Chivumbulutso 1:14

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Miy 20:29; Da 7:9
  • +Chv 19:12

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 25

Chivumbulutso 1:15

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 2:18
  • +Chv 1:10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 25-26

Chivumbulutso 1:16

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 1:20
  • +Yes 49:2
  • +Mt 17:2

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    10/15/2012, tsa. 14

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 26-27, 28-29

Chivumbulutso 1:17

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mt 17:7
  • +Mac 26:23; Akl 1:18; Chv 1:5
  • +Yoh 5:21; 6:40; Chv 2:8

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Nsanja ya Olonda,

    1/15/2009, ptsa. 30-31

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 26-28

Chivumbulutso 1:18

Mawu a M'munsi

  • *

    Onani Zakumapeto 5.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Lu 24:5; 1Ak 15:45
  • +Aro 5:6; 1Pe 3:18
  • +Aro 6:9; 1Ti 6:16; Ahe 7:24
  • +Yob 38:17; Sl 9:13
  • +Yes 38:10; Mt 16:18; Yoh 6:54; 11:25

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 27-28

    Lambirani Mulungu, ptsa. 83-84

Chivumbulutso 1:19

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 4:1; 22:6

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 24

Chivumbulutso 1:20

Mawu a M'munsi

  • *

    Kapena kuti, “amithenga.”

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 1:16
  • +Chv 1:12
  • +Mt 5:16; Afi 2:15

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Utumiki Komanso Moyo Wathu,

    11/2019, tsa. 5

    Nsanja ya Olonda,

    10/15/2012, tsa. 14

    9/15/2010, tsa. 27

    1/15/2009, tsa. 30

    4/1/2007, tsa. 27

    5/15/2003, ptsa. 10-11

    3/15/2002, tsa. 14

    10/1/1988, tsa. 17

    8/1/1987, ptsa. 17-18

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 28-29, 136

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

Chiv. 1:11Ak 14:6; Aga 1:12
Chiv. 1:1Da 2:28; Yoh 12:49
Chiv. 1:1Amo 3:7; Chv 7:3; 22:6
Chiv. 1:1Chv 1:19
Chiv. 1:1Chv 22:16
Chiv. 1:1Mac 2:22
Chiv. 1:1Mt 10:2; Mko 1:19; Yoh 21:20
Chiv. 1:2Chv 1:9
Chiv. 1:2Chv 22:20
Chiv. 1:3Sl 1:2; 1Ti 4:13
Chiv. 1:3Chv 22:18
Chiv. 1:3Lu 11:28; Yak 1:22
Chiv. 1:3Da 8:19; Chv 22:10
Chiv. 1:3Yoh 13:17
Chiv. 1:4Chv 1:11
Chiv. 1:4Eks 3:14; Chv 1:8; 4:8; 11:17
Chiv. 1:4Chv 4:5
Chiv. 1:5Sl 89:37; Chv 3:14
Chiv. 1:5Akl 1:18
Chiv. 1:5Sl 89:27; 1Ti 6:15; Chv 19:16
Chiv. 1:5Yoh 15:9
Chiv. 1:5Ahe 9:14; 1Pe 1:19; 1Yo 1:7
Chiv. 1:6Eks 19:6; Lu 22:29
Chiv. 1:61Pe 2:5; Chv 5:10; 20:6
Chiv. 1:61Ti 6:16
Chiv. 1:7Da 7:13; Mt 26:64; Mko 13:26; Mac 1:11; 1At 4:17; Chv 14:14
Chiv. 1:7Aef 1:18
Chiv. 1:7Mt 27:49
Chiv. 1:7Mt 24:30
Chiv. 1:8Yes 48:12; Chv 21:6; 22:13
Chiv. 1:8Chv 1:4
Chiv. 1:8Ge 17:1; Eks 6:3
Chiv. 1:9Mt 24:9; Ahe 10:33; Chv 2:10
Chiv. 1:9Aro 8:17
Chiv. 1:9Lu 12:32
Chiv. 1:9Mt 10:22; 2Ti 2:12
Chiv. 1:9Mac 1:8
Chiv. 1:101Mb 28:12; Mt 22:43
Chiv. 1:10Eze 40:2; 2Ak 12:2
Chiv. 1:101Ak 1:8; 5:5
Chiv. 1:10Chv 1:15
Chiv. 1:11Hab 2:2
Chiv. 1:11Chv 1:4
Chiv. 1:11Aef 1:1; Chv 2:1
Chiv. 1:11Chv 2:8
Chiv. 1:11Chv 2:12
Chiv. 1:11Mac 16:14; Chv 2:18
Chiv. 1:11Chv 3:1
Chiv. 1:11Chv 3:7
Chiv. 1:11Akl 4:16; Chv 3:14
Chiv. 1:122Mb 4:7; Chv 1:20
Chiv. 1:13Da 7:13; Chv 14:14
Chiv. 1:14Miy 20:29; Da 7:9
Chiv. 1:14Chv 19:12
Chiv. 1:15Chv 2:18
Chiv. 1:15Chv 1:10
Chiv. 1:16Chv 1:20
Chiv. 1:16Yes 49:2
Chiv. 1:16Mt 17:2
Chiv. 1:17Mt 17:7
Chiv. 1:17Mac 26:23; Akl 1:18; Chv 1:5
Chiv. 1:17Yoh 5:21; 6:40; Chv 2:8
Chiv. 1:18Lu 24:5; 1Ak 15:45
Chiv. 1:18Aro 5:6; 1Pe 3:18
Chiv. 1:18Aro 6:9; 1Ti 6:16; Ahe 7:24
Chiv. 1:18Yob 38:17; Sl 9:13
Chiv. 1:18Yes 38:10; Mt 16:18; Yoh 6:54; 11:25
Chiv. 1:19Chv 4:1; 22:6
Chiv. 1:20Chv 1:16
Chiv. 1:20Chv 1:12
Chiv. 1:20Mt 5:16; Afi 2:15
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano (nwt)
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
  • 14
  • 15
  • 16
  • 17
  • 18
  • 19
  • 20
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Chivumbulutso 1:1-20

Chivumbulutso

1 Chivumbulutso+ choperekedwa ndi Yesu Khristu, chimene Mulungu anamupatsa,+ kuti aonetse akapolo ake+ zinthu zimene ziyenera kuchitika posachedwapa.+ Yesuyo anatumiza mngelo wake+ kuti adzapereke Chivumbulutsocho mwa zizindikiro+ kwa kapolo wake Yohane.+ 2 Yohaneyo anachitira umboni mawu a Mulungu,+ ndiponso umboni umene Yesu Khristu anapereka,+ kutanthauza zonse zimene anaona. 3 Wodala+ ndi munthu amene amawerenga mokweza,+ ndiponso anthu amene akumva mawu a ulosi umenewu,+ komanso amene akusunga zolembedwamo,+ pakuti nthawi yoikidwiratu ili pafupi.+

4 Ine Yohane, ndikulembera mipingo 7+ ya m’chigawo cha Asia.

Kukoma mtima kwakukulu, ndi mtendere zikhale nanu kuchokera kwa “Iye amene alipo, amene analipo, ndi amene akubwera,”+ ndiponso kuchokera kwa mizimu 7+ yokhala pamaso pa mpando wake wachifumu. 5 Komanso, kuchokera kwa Yesu Khristu, “Mboni Yokhulupirika,”+ “Woyamba kubadwa kuchokera kwa akufa,”+ ndiponso “Wolamulira wa mafumu a dziko lapansi.”+

Kwa iye amene amatikonda,+ amenenso anatimasula ku machimo athu ndi magazi ake enieniwo,+ 6 n’kutipanga kukhala mafumu+ ndi ansembe+ kwa Mulungu wake ndi Atate wake, kwa iyeyo kukhale ulemerero ndi mphamvu kwamuyaya.+ Ame.

7 Taonani! Akubwera ndi mitambo,+ ndipo diso lililonse lidzamuona,+ ngakhalenso anthu amene anamulasa.+ Ndipo mafuko onse a padziko lapansi adzadziguguda pachifuwa ndi chisoni chifukwa cha iye.+ Ame.

8 “Ine ndine Alefa ndi Omega,”*+ akutero Yehova Mulungu, “Iye amene alipo, amene analipo, ndi amene akubwera,+ Wamphamvuyonse.”+

9 Ine Yohane, m’bale wanu ndi wogawana nanu masautso+ a Yesu,+ mu ufumu+ ndi m’kupirira,+ ndinali pachilumba cha Patimo chifukwa cholankhula za Mulungu ndi kuchitira umboni za Yesu.+ 10 Mwa mzimu,+ ndinapezeka kuti ndili+ m’tsiku la Ambuye,+ ndipo kumbuyo kwanga ndinamva mawu amphamvu+ ngati kulira kwa lipenga. 11 Mawuwo anali akuti: “Zimene uone, lemba+ mumpukutu ndi kuutumiza kumipingo 7+ yotsatirayi: wa ku Efeso,+ wa ku Simuna,+ wa ku Pegamo,+ wa ku Tiyatira,+ wa ku Sade,+ wa ku Filadefiya,+ ndi wa ku Laodikaya.”+

12 Ndinacheuka kuti ndione, kuti ndani amene anali kundilankhula. Nditacheuka, ndinaona zoikapo nyale 7 zagolide.+ 13 Pakati pa zoikapo nyalezo, panali wina wooneka ngati mwana wa munthu+ atavala chovala chofika kumapazi, atamanga lamba wagolide pachifuwa. 14 Komanso, mutu ndi tsitsi lake zinali zoyera+ ngati ubweya wa nkhosa woyera, zoyera kwambiri kuti mbee! Ndipo maso ake anali ngati lawi la moto.+ 15 Mapazi ake anali ngati mkuwa woyengedwa+ bwino ukamanyezimira m’ng’anjo, ndipo mawu+ ake anali ngati mkokomo wa madzi ambiri. 16 M’dzanja lake lamanja anali ndi nyenyezi 7.+ M’kamwa mwake munali kutuluka lupanga lalitali, lakuthwa konsekonse.+ Nkhope yake inali yowala ngati dzuwa limene likuwala kwambiri.+ 17 Nditamuona, ndinagwa pamapazi ake ngati kuti ndafa.

Ndipo anandigwira ndi dzanja lake lamanja ndi kundiuza kuti: “Usachite mantha.+ Ine ndine Woyamba+ ndi Wotsiriza,+ 18 ndiponso wamoyo.+ Ndinali wakufa,+ koma taona, ndili ndi moyo kwamuyaya,+ ndipo ndili ndi makiyi a imfa+ ndi a Manda.*+ 19 Choncho lemba zimene waona, zimene zikuchitika panopa, ndi zimene zidzachitike pambuyo pa zimenezi.+ 20 Koma za chinsinsi chopatulika cha nyenyezi 7,+ zimene waona m’dzanja langa lamanja, ndi za chinsinsi cha zoikapo nyale 7 zagolide,+ tanthauzo lake ndi ili: Nyenyezi 7, zikuimira angelo* a mipingo 7, ndipo zoikapo nyale 7, zikuimira mipingo 7.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena