2 Mbiri 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako anapanga zoikapo nyale+ 10 zagolide zofanana,+ n’kuziika m’kachisi. Anaika zisanu mbali ya kudzanja lamanja, zisanu mbali ya kumanzere.+ Chivumbulutso 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma za chinsinsi chopatulika cha nyenyezi 7,+ zimene waona m’dzanja langa lamanja, ndi za chinsinsi cha zoikapo nyale 7 zagolide,+ tanthauzo lake ndi ili: Nyenyezi 7, zikuimira angelo* a mipingo 7, ndipo zoikapo nyale 7, zikuimira mipingo 7.+
7 Kenako anapanga zoikapo nyale+ 10 zagolide zofanana,+ n’kuziika m’kachisi. Anaika zisanu mbali ya kudzanja lamanja, zisanu mbali ya kumanzere.+
20 Koma za chinsinsi chopatulika cha nyenyezi 7,+ zimene waona m’dzanja langa lamanja, ndi za chinsinsi cha zoikapo nyale 7 zagolide,+ tanthauzo lake ndi ili: Nyenyezi 7, zikuimira angelo* a mipingo 7, ndipo zoikapo nyale 7, zikuimira mipingo 7.+