Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 37:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Kenako anapanga choikapo nyale+ chagolide woyenga bwino. Chimenechi chinali chosula. Choikapo nyalechi chinali ndi nthambi m’mbali mwake, ndiponso chinali ndi masamba ofunga duwa, mfundo ndi maluwa.+

  • 2 Mbiri 4:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 ndi zoikapo nyale+ ndi nyale zake+ zagolide woyenga bwino, zoti aziziyatsa m’chipinda chamkati+ mogwirizana ndi lamulo.

  • Zekariya 4:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Kenako anandifunsa kuti: “Ukuona chiyani?”+

      Ine ndinayankha kuti: “Ndikuona choikapo nyale chagolide yekhayekha.+ Pamwamba pake pali mbale yolowa. Choikapo nyalecho chili ndi nyale 7, inde, nyale 7.+ Nyale zimene zili pachoikapo nyalecho, zili ndi mapaipi 7.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena