Ekisodo 37:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kenako anapanga choikapo nyale+ chagolide woyenga bwino. Chimenechi chinali chosula. Choikapo nyalechi chinali ndi nthambi m’mbali mwake, ndiponso chinali ndi masamba ofunga duwa, mfundo ndi maluwa.+ 1 Mafumu 7:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Anapanganso zoikapo nyale+ zagolide woyenga bwino,+ n’kukaziika pafupi ndi chipinda chamkati, zisanu mbali ya kudzanja lamanja, zisanu mbali ya kumanzere. Ndiponso anapanga maluwa+ agolide, nyale+ zagolide, zopanira+ zagolide zozimitsira nyale,
17 Kenako anapanga choikapo nyale+ chagolide woyenga bwino. Chimenechi chinali chosula. Choikapo nyalechi chinali ndi nthambi m’mbali mwake, ndiponso chinali ndi masamba ofunga duwa, mfundo ndi maluwa.+
49 Anapanganso zoikapo nyale+ zagolide woyenga bwino,+ n’kukaziika pafupi ndi chipinda chamkati, zisanu mbali ya kudzanja lamanja, zisanu mbali ya kumanzere. Ndiponso anapanga maluwa+ agolide, nyale+ zagolide, zopanira+ zagolide zozimitsira nyale,