Ekisodo 37:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndiyeno anachipangira nyale 7, zopanira zake zozimitsira nyale ndi mbale zake zoikamo phulusa la zingwe za nyale. Zonsezi zinali zagolide woyenga bwino.+ Numeri 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Lankhula ndi Aroni, unene kuti, ‘Ukayatsa nyale 7 zija, ziziunika malo apatsogolo pa choikapo nyalecho.’”+ 2 Mbiri 29:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anatseka zitseko+ za khonde, anazimitsa nyale,+ ndiponso anasiya kupsereza zofukiza+ ndi kupereka nsembe zopsereza kwa Mulungu wa Isiraeli m’malo oyera.+ Luka 12:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 “Mangani m’chiuno mwanu+ ndipo nyale+ zanu zikhale chiyakire.
23 Ndiyeno anachipangira nyale 7, zopanira zake zozimitsira nyale ndi mbale zake zoikamo phulusa la zingwe za nyale. Zonsezi zinali zagolide woyenga bwino.+
2 “Lankhula ndi Aroni, unene kuti, ‘Ukayatsa nyale 7 zija, ziziunika malo apatsogolo pa choikapo nyalecho.’”+
7 Anatseka zitseko+ za khonde, anazimitsa nyale,+ ndiponso anasiya kupsereza zofukiza+ ndi kupereka nsembe zopsereza kwa Mulungu wa Isiraeli m’malo oyera.+