Ekisodo 25:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Ndipo uchipangire nyale 7. Nyalezo ziziyatsidwa kuti ziziunikira patsogolo pake.+ Ekisodo 25:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Zopanira zake zozimitsira nyale ndi mbale zake zoikamo phulusa la zingwe za nyale, zikhale zagolide woyenga bwino.+ Numeri 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Lankhula ndi Aroni, unene kuti, ‘Ukayatsa nyale 7 zija, ziziunika malo apatsogolo pa choikapo nyalecho.’”+
38 Zopanira zake zozimitsira nyale ndi mbale zake zoikamo phulusa la zingwe za nyale, zikhale zagolide woyenga bwino.+
2 “Lankhula ndi Aroni, unene kuti, ‘Ukayatsa nyale 7 zija, ziziunika malo apatsogolo pa choikapo nyalecho.’”+