Ekisodo 37:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndiyeno anachipangira nyale 7, zopanira zake zozimitsira nyale ndi mbale zake zoikamo phulusa la zingwe za nyale. Zonsezi zinali zagolide woyenga bwino.+ Numeri 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno azitenga nsalu yabuluu n’kuphimbira choikapo nyale,+ pamodzi ndi nyale zake,+ zopanira zake zozimitsira nyale,+ zoikamo phulusa la zingwe za nyale,+ ndi ziwiya zake zonse+ zosungiramo mafuta ogwiritsa ntchito nthawi zonse.
23 Ndiyeno anachipangira nyale 7, zopanira zake zozimitsira nyale ndi mbale zake zoikamo phulusa la zingwe za nyale. Zonsezi zinali zagolide woyenga bwino.+
9 Ndiyeno azitenga nsalu yabuluu n’kuphimbira choikapo nyale,+ pamodzi ndi nyale zake,+ zopanira zake zozimitsira nyale,+ zoikamo phulusa la zingwe za nyale,+ ndi ziwiya zake zonse+ zosungiramo mafuta ogwiritsa ntchito nthawi zonse.