Ekisodo 25:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Ndipo uchipangire nyale 7. Nyalezo ziziyatsidwa kuti ziziunikira patsogolo pake.+ Ekisodo 40:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndipo anayatsa nyalezo+ pamaso pa Yehova, monga mmene Yehova analamulira Mose. Levitiko 24:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Lamula ana a Isiraeli kuti akupezere mafuta ounikira+ oyenga bwino kwambiri a maolivi, kuti nyale iziyaka nthawi zonse.+
2 “Lamula ana a Isiraeli kuti akupezere mafuta ounikira+ oyenga bwino kwambiri a maolivi, kuti nyale iziyaka nthawi zonse.+