Ekisodo 40:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndipo anayatsa nyalezo+ pamaso pa Yehova, mogwirizana ndi zimene Yehova analamula Mose.