Ekisodo 25:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Muchipangire nyale 7 ndipo nyalezo zikayatsidwa ziziunikira malo amene ali patsogolo pake.+ Ekisodo 37:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kenako anachipangira nyale 7,+ zopanira zake zozimitsira nyale ndi mbale zake zoikamo phulusa la zingwe za nyale. Zonsezi zinali zagolide woyenga bwino.
23 Kenako anachipangira nyale 7,+ zopanira zake zozimitsira nyale ndi mbale zake zoikamo phulusa la zingwe za nyale. Zonsezi zinali zagolide woyenga bwino.