Ekisodo 40:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndipo anayatsa nyalezo+ pamaso pa Yehova, monga mmene Yehova analamulira Mose.