Ekisodo 25:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “Kenako upange choikapo nyale chagolide woyenga bwino. Chimenechi chikhale chosula.+ Choikapo nyalecho chikhale ndi tsinde, nthambi, masamba ofunga duwa, mfundo ndi maluwa. 1 Mafumu 7:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Anapanganso zoikapo nyale+ zagolide woyenga bwino,+ n’kukaziika pafupi ndi chipinda chamkati, zisanu mbali ya kudzanja lamanja, zisanu mbali ya kumanzere. Ndiponso anapanga maluwa+ agolide, nyale+ zagolide, zopanira+ zagolide zozimitsira nyale, Chivumbulutso 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndinacheuka kuti ndione, kuti ndani amene anali kundilankhula. Nditacheuka, ndinaona zoikapo nyale 7 zagolide.+
31 “Kenako upange choikapo nyale chagolide woyenga bwino. Chimenechi chikhale chosula.+ Choikapo nyalecho chikhale ndi tsinde, nthambi, masamba ofunga duwa, mfundo ndi maluwa.
49 Anapanganso zoikapo nyale+ zagolide woyenga bwino,+ n’kukaziika pafupi ndi chipinda chamkati, zisanu mbali ya kudzanja lamanja, zisanu mbali ya kumanzere. Ndiponso anapanga maluwa+ agolide, nyale+ zagolide, zopanira+ zagolide zozimitsira nyale,
12 Ndinacheuka kuti ndione, kuti ndani amene anali kundilankhula. Nditacheuka, ndinaona zoikapo nyale 7 zagolide.+