Yeremiya 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno Yehova anapitirizabe kulankhula nane, ndipo anati: “Ukuona chiyani Yeremiya?” Ine ndinayankha kuti: “Ndikuona mphukira ya mtengo wa amondi.”* Zekariya 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye anandifunsa kuti: “Ukuona chiyani?”+ Ine ndinayankha kuti: “Ndikuona mpukutu ukuuluka. Mpukutuwo ndi wautali mikono* 20 ndipo m’lifupi mwake ndi wautali mikono 10.”
11 Ndiyeno Yehova anapitirizabe kulankhula nane, ndipo anati: “Ukuona chiyani Yeremiya?” Ine ndinayankha kuti: “Ndikuona mphukira ya mtengo wa amondi.”*
2 Iye anandifunsa kuti: “Ukuona chiyani?”+ Ine ndinayankha kuti: “Ndikuona mpukutu ukuuluka. Mpukutuwo ndi wautali mikono* 20 ndipo m’lifupi mwake ndi wautali mikono 10.”