2 Kenako anandifunsa kuti: “Ukuona chiyani?”+
Ine ndinayankha kuti: “Ndikuona choikapo nyale chagolide yekhayekha.+ Pamwamba pake pali mbale yolowa. Choikapo nyalecho chili ndi nyale 7, inde, nyale 7.+ Nyale zimene zili pachoikapo nyalecho, zili ndi mapaipi 7.