Aroma 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tikudziwa kuti pamene tsopano Khristu waukitsidwa kwa akufa,+ sadzafanso.+ Imfa sikuchitanso ufumu pa iye. 1 Timoteyo 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iye yekha ndiye amene ali ndi moyo wosakhoza kufa,+ amene amakhala m’kuwala kosafikirika.+ Palibe munthu ndi mmodzi yemwe amene anamuonapo kapena amene angamuone.+ Iye apatsidwe ulemu+ ndipo mphamvu zake zikhalebe kosatha. Ame. Aheberi 7:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma iye chifukwa chokhala ndi moyo kosatha,+ palibe omulowa m’malo pa unsembe wake.
9 Tikudziwa kuti pamene tsopano Khristu waukitsidwa kwa akufa,+ sadzafanso.+ Imfa sikuchitanso ufumu pa iye.
16 Iye yekha ndiye amene ali ndi moyo wosakhoza kufa,+ amene amakhala m’kuwala kosafikirika.+ Palibe munthu ndi mmodzi yemwe amene anamuonapo kapena amene angamuone.+ Iye apatsidwe ulemu+ ndipo mphamvu zake zikhalebe kosatha. Ame.