Aheberi 7:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma popeza iye adzakhala ndi moyo mpaka kalekale,+ palibe wansembe amene adzamulowe mʼmalo.