Aheberi 7:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma iye chifukwa chokhala ndi moyo kosatha,+ palibe omulowa m’malo pa unsembe wake.